Surah: Al-Humazah (Qur'an Ch 104) [Khalaf 'An Hamzah]
Reciter: Shaykh Shaykh Abdul Rashid Ali Sufi (Somalia)
Translation: Shaykh Khalid Ibrahim Pitala (Malawi)
M’surayi muli lonjezo la chilango choopsa kwa munthu amene ali ndi chizolowezi chojeda ndi kunyoza anthu, powalozera ndi maso kapena kuyankhula. Ndiponso amene amati akasonkhanitsa chuma amachiwerengera pafupipafupi mokhumbiza ena uku akuganizira kuti chumacho chimkhazika muyaya.
Ещё видео!